KI-Songgenerator Textgenerator Preise Meine Songs

Pita

Song generated By ✨Song.do

Song Cover
v1

@ Serene Oht

2026-05-21 20:03:36

Liedtexte

Verse 1
Lalika za Yahuwah mfumu
Dziko lonse limudziwetu
Lalika za Atate wathu
Aliyense anve za yiye
Lalika za Yahuwah mfumu
Dziko lonse limudziwetu
Lalika za Atate wathu
Aliyense anve za yiye

Chorus:
Pita ku mtunda wukalalike
Pita kuchigwa wukalalike
Pita mtawuni wukalalike
Pita kumudzinso
Pita kumpoto wukalalike
Pita kumwela wukalalike
Pita kuvuma wukalalike
Pita kuzambwenso

Verse 2
Lalika za chikondi chake
Choposa zonse za mdzikoli
Lalika za chipulumutso
Chobwela mwa Mwana wakeyo
Lalika kwa wosawukawo
Ndi olemedwa mumtimamo
Kuti Yahuwah aali nawo
Amapatsa moyo weniweni

Chorus:
Pita ku mtunda wukalalike
Pita kuchigwa wukalalike
Pita mtawuni wukalalike
Pita kumudzinso
Pita kumpoto wukalalike
Pita kumwela wukalalike
Pita kuvuma wukalalike
Pita kuzambwenso

Verse 3
Lalika kuti nthawi yatha
Ndipo anthu alape lelo
Lalika za wufumu wake
Wosatha nthawi zonsezotu
Lalika mwa mphamvu yake
usawope pena kutopa
Yahuwah adzakhala nawe
Pokalalika mawu ake

Chorus:

Pita ku mtunda wukalalike
Pita kuchigwa wukalalike
Pita mtawuni wukalalike
Pita kumudzinso
Pita kumpoto wukalalike
Pita kumwela wukalalike
Pita kuvuma wukalalike
Pita kuzambwenso

Pita ku mtunda
Pita ku chigwa
Pita mtawuni
Pita kumudzinso
Pita kumpoto
Pita kumwela
Pita kuvuma
Pita kuzambwenso

Pita ku mtunda wukalalike
Pita kuchigwa wukalalike
Pita mtawuni wukalalike
Pita kumudzinso
Pita kumpoto wukalalike
Pita kumwela wukalalike
Pita kuvuma wukalalike
Pita kuzambwenso

Musikstil

1980 Choir, SATB verses and chorus, piano only