AI Song Generator Lyrics Generator Vocal Remover Pricing My Songs

Chikondi

Song generated By ✨Song.do

Song Cover
v5 Lite

@ Yusy One

2026-11-26 23:02:07

Lyrics

(Intro)
Ndine, stivi juwawu

(Thuboy beats)

(Chorus)
Sindizayiwala chikondi chapafoni.
Kungopasana moni.
Koma osanverana chisoni.
Sindizapangaso chikondi chapafoni.
Kunamizila moni.
Ndikuzinvera chisoni.

(Verse)
Osazapanga, chikondi chani.
Kumangopasana moni.
Bola kumangonvera matoni.
Munthune ndazionaine.
Zikondi zamufoni ine.
Pena amabweraa!.
Ngati wachikondi kufuna kukubera.
Ukatumiza eyatayimu.
Amakuyankha, kamodzi kokha.
Tili bwino kaya inu.
(Kenako ziiiiii)
After two hours.
Ndinali bize, ndimachapa, komano paize.

Or mafoto amatumizila Ena.
Inuyo mukugona.
Data akatha.
Amati ayilavu yu.
Chikondi chapafonii.
Sindizaiwala.

(Chorus)
Sindizayiwala chikondi chapafoni.
Kungopasana moni.
Koma osanverana chisoni.
Sindizapangaso chikondi chapafoni.
Kunamizila moni.
Ndikuzinvera chisoni.

(Verse)
Amadzayimba foni.
Iwe kuwayankha .
(kenako ziiii)
Koma chikondi chapafoni.
Bola kumangonvera matoni.

(Chorus)
Sindizayiwala chikondi chapafoni.
Kungopasana moni.
Koma osanverana chisoni.
Sindizapangaso chikondi chapafoni.
Kunamizila moni.
Ndikuzinvera chisoni.

(Last Intro)
(Nkuzi mix music)
(Yuze, yuze, yuze)

Style of Music

Malawian afro pip, afro R&B, Amapiano
[Instrumental Break]
[Sudden Silence]
[Whispered voice: kenako ziiii]
[Pause], Male Vocals