AI 歌曲產生器 歌詞產生器 價格 我的歌曲

Dziko la lonjezolo

Song generated By ✨Song.do

Song Cover
v1

@ Sydney Chimgwede

2026-08-04 03:37:20

歌詞

Ndikayang'ana kutali
Mtima wanga umazama
Ndimalota za tsiku lina
Nditafika kwathuko
Kopanda misozi
Kopanda ululu
Yahuah adzandilandila
Mu dziko la lonjezolo

Chorus
Tidzakhala mu mtendele (Shalom)
Tidzakhala ndi chimwemwe (shalom)
Tidzadya zipatso zabwino
Tidzamwa mu mitsinje
Tidzayimba mosatopa (HaleluYah)
Tidzaseka limodzi tonse (HaleluYah)
Yahuah adzakhala nafe
Mu dziko la lonjezolo

Verse 2
Minda yobiliwira
Mitengo idzabala
Mitsinjenso yodzaza
Madzi oyela bwino
Ana adzathamanga
Akulu adzaseka
Sipadzakhala kulila
Mu dziko la lonjezolo

Chorus
Tidzakhala mu mtendele (Shalom)
Tidzakhala ndi chimwemwe (shalom)
Tidzadya zipatso zabwino
Tidzamwa mu mitsinje
Tidzayimba mosatopa (HaleluYah)
Tidzaseka limodzi tonse (HaleluYah)
Yahuah adzakhala nafe
Mu dziko la lonjezolo

Bridge
Pamene tili tikuyenda
Tiyembekeza tsikulo
Chiyembekezo sidzatha
Yahuah sasinthanso
Tiyeni tilimbike
Tisabwelele m'mbuyo
Posachedwa tidzafika
Mu dziko la lonjezolo

Final Chorus
Tidzakhala mu mtendele (Shalom)
Tidzakhala ndi chimwemwe (shalom)
Tidzadya zipatso zabwino
Tidzamwa mu mitsinje
Tidzayimba mosatopa (HaleluYah)
Tidzaseka limodzi tonse (HaleluYah)
Yahuah adzakhala nafe
Mu dziko la lonjezolo

音樂風格

1980 country gospel duet